Luka 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Watsitsa anthu amphamvu+ zawo pamipando yachifumu, ndipo wakweza anthu wamba.+ 1 Petulo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho dzichepetseni pansi pa dzanja lamphamvu la Mulungu, kuti adzakukwezeni m’nthawi yake.+