Yobu 38:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi unali kuti pamene ndinkaika maziko a dziko lapansi?+Ndiuze ngati uli womvetsa zinthu. Salimo 102:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+