Salimo 18:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndidzathamangitsa adani anga ndi kuwapeza,Ndipo sindidzabwerera kufikira nditawawononga onse.+