1 Samueli 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Eli anali wokalamba kwambiri ndipo anamva+ zonse zimene ana ake anali kuchitira+ Aisiraeli onse, komanso anamva kuti anali kugona ndi akazi+ otumikira pakhomo la chihema chokumanako.+ Miyambo 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwana wopusa amakhumudwitsa bambo ake,+ ndipo amamvetsa chisoni mayi ake amene anam’bereka.+
22 Ndiyeno Eli anali wokalamba kwambiri ndipo anamva+ zonse zimene ana ake anali kuchitira+ Aisiraeli onse, komanso anamva kuti anali kugona ndi akazi+ otumikira pakhomo la chihema chokumanako.+