Deuteronomo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Arefai+ anali kuonedwanso ngati Aanaki,+ ndipo Amowabu anali kutcha Arefaiwo kuti Aemi.