2 Samueli 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita nthawi, Davide anauzidwa+ zimene Rizipa mwana wa Aya, mdzakazi wa Sauli anachita.