-
Oweruza 8:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kenako, Gidiyoni anafika ku Yorodano n’kuwoloka mtsinjewo pamodzi ndi amuna 300 amene anali nawo aja, ali otopa koma akuthamangitsabe adaniwo.
-