1 Mbiri 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtsogoleri wa 7, wa mwezi wa 7, anali Helezi+ Mpeloni,+ wochokera mwa ana a Efuraimu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
10 Mtsogoleri wa 7, wa mwezi wa 7, anali Helezi+ Mpeloni,+ wochokera mwa ana a Efuraimu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.