Numeri 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uwerenge+ khamu lonse la ana a Isiraeli malinga ndi mabanja awo, potsata nyumba za makolo awo, n’kulemba mayina awo. Uwerenge amuna onse, mmodzi ndi mmodzi.
2 “Uwerenge+ khamu lonse la ana a Isiraeli malinga ndi mabanja awo, potsata nyumba za makolo awo, n’kulemba mayina awo. Uwerenge amuna onse, mmodzi ndi mmodzi.