2 Mafumu 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yehoyada anachita pangano+ pakati pa Yehova,+ mfumu,+ ndi anthu, kuti anthuwo azisonyeza kuti ndi anthu a Yehova. Anachitanso pangano pakati pa mfumu ndi anthuwo.+
17 Kenako Yehoyada anachita pangano+ pakati pa Yehova,+ mfumu,+ ndi anthu, kuti anthuwo azisonyeza kuti ndi anthu a Yehova. Anachitanso pangano pakati pa mfumu ndi anthuwo.+