Salimo 89:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inenso ndidzamuika kukhala mwana woyamba kubadwa,+Ndiponso mfumu yaikulu pa mafumu onse a padziko lapansi.+
27 Inenso ndidzamuika kukhala mwana woyamba kubadwa,+Ndiponso mfumu yaikulu pa mafumu onse a padziko lapansi.+