1 Mbiri 16:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pambuyo pake anthu onse ananyamuka, ndipo aliyense anapita kunyumba kwake.+ Nayenso Davide anapita kunyumba kwake n’kukadalitsa banja lake.
43 Pambuyo pake anthu onse ananyamuka, ndipo aliyense anapita kunyumba kwake.+ Nayenso Davide anapita kunyumba kwake n’kukadalitsa banja lake.