6 Pa nthawi yonse imene ndinali kuyendayenda+ pakati pa Isiraeli yense, kodi ndinalankhulapo n’kamodzi komwe kwa woweruza aliyense wa Isiraeli, amene ndinalamula kutsogolera anthu anga, mawu akuti, ‘N’chifukwa chiyani anthu inu simunandimangire nyumba ya mitengo ya mkungudza?’”’+