1 Mbiri 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho dalitsani nyumba ya mtumiki wanu kuti ikhazikike pamaso panu mpaka kalekale.+ Pakuti inu Yehova mwadalitsa nyumba ya mtumiki wanu, ndipo yadalitsika mpaka kalekale.”+
27 Choncho dalitsani nyumba ya mtumiki wanu kuti ikhazikike pamaso panu mpaka kalekale.+ Pakuti inu Yehova mwadalitsa nyumba ya mtumiki wanu, ndipo yadalitsika mpaka kalekale.”+