1 Mbiri 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Tou, mfumu ya Hamati,+ atamva kuti Davide wapha gulu lonse lankhondo la Hadadezeri+ mfumu ya Zoba,
9 Tsopano Tou, mfumu ya Hamati,+ atamva kuti Davide wapha gulu lonse lankhondo la Hadadezeri+ mfumu ya Zoba,