Rute 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Boazi anati: “Ukadzagula mundawo kwa Naomi, ndiye kuti waugulanso kwa Rute Mmowabu, amene mwamuna wake anamwalira, kuti dzina la mwamuna wakeyo libwerere pacholowa chake.”+
5 Kenako Boazi anati: “Ukadzagula mundawo kwa Naomi, ndiye kuti waugulanso kwa Rute Mmowabu, amene mwamuna wake anamwalira, kuti dzina la mwamuna wakeyo libwerere pacholowa chake.”+