2 Samueli 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi amuna 20,000 oyenda pansi+ a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula*+ mahatchi onse a magaleta+ kusiyapo mahatchi a magaleta okwana 100.
4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi amuna 20,000 oyenda pansi+ a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula*+ mahatchi onse a magaleta+ kusiyapo mahatchi a magaleta okwana 100.