1 Akorinto 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 N’chifukwa chake amene akuyesa kuti ali chilili asamale kuti asagwe.+ Yakobo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu aliyense amayesedwa mwa kukopedwa ndi kukodwa m’chilakolako chake.+