2 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni.
9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni.