Miyambo 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wosasunthika pachilungamo adzapeza moyo,+ koma munthu wofunafuna zoipa adzafa.+