2 Samueli 13:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo Yehonadabu+ anauza mfumu kuti: “Taonani! Ana a mfumu akubwera. Zachitika monga mwa mawu a mtumiki wanu.”+
35 Pamenepo Yehonadabu+ anauza mfumu kuti: “Taonani! Ana a mfumu akubwera. Zachitika monga mwa mawu a mtumiki wanu.”+