Yohane 11:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Pa chifukwa chimenechi, Yesu sanalinso kuyendayenda moonekera+ kwa Ayuda.+ Koma anachoka kumeneko ndi kupita kudera lina lapafupi ndi chipululu, mumzinda wotchedwa Efuraimu.+ Ndipo anakhala kumeneko pamodzi ndi ophunzira ake.
54 Pa chifukwa chimenechi, Yesu sanalinso kuyendayenda moonekera+ kwa Ayuda.+ Koma anachoka kumeneko ndi kupita kudera lina lapafupi ndi chipululu, mumzinda wotchedwa Efuraimu.+ Ndipo anakhala kumeneko pamodzi ndi ophunzira ake.