2 Samueli 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chotero Abisalomu anathawa ndi kupita ku Gesuri+ ndipo anakhala kumeneko zaka zitatu. Miyambo 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wolemedwa ndi mlandu wokhetsa magazi a munthu adzakhala wothawathawa mpaka kumanda.+ Anthu asamugwire n’cholinga choti amuletse.
17 Munthu wolemedwa ndi mlandu wokhetsa magazi a munthu adzakhala wothawathawa mpaka kumanda.+ Anthu asamugwire n’cholinga choti amuletse.