Machitidwe 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Waloledwa kulankhula mbali yako.” Pamenepo Paulo anatambasula dzanja lake+ ndi kuyamba kulankhula modziteteza kuti:+
26 Ndiyeno Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Waloledwa kulankhula mbali yako.” Pamenepo Paulo anatambasula dzanja lake+ ndi kuyamba kulankhula modziteteza kuti:+