2 Samueli 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ine mtumiki wanu ndinaganiza kuti, ‘Mawu a mbuyanga mfumu andipatsa mpumulo.’ Pakuti inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, wokhoza kusiyanitsa chabwino ndi choipa.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.”
17 ine mtumiki wanu ndinaganiza kuti, ‘Mawu a mbuyanga mfumu andipatsa mpumulo.’ Pakuti inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, wokhoza kusiyanitsa chabwino ndi choipa.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.”