Miyambo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa mapazi awo amathamangira zoipa,+ ndipo iwo amafulumira kukakhetsa magazi.+