2 Samueli 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mfumu inauza Zadoki kuti: “Tenga likasa+ la Mulungu woona ndi kubwerera nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandibwezeretsa mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+ Salimo 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa mwandiweruzira mlandu wanga ndi dandaulo langa.+Mwakhala pampando wachifumu ndipo mukuweruza mwachilungamo.+
25 Ndiyeno mfumu inauza Zadoki kuti: “Tenga likasa+ la Mulungu woona ndi kubwerera nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandibwezeretsa mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+
4 Chifukwa mwandiweruzira mlandu wanga ndi dandaulo langa.+Mwakhala pampando wachifumu ndipo mukuweruza mwachilungamo.+