Numeri 14:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Musapite kumeneko chifukwa Yehova sali nanu. Adani anuwo akakugonjetsani.+