Ezekieli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo ukachenjeza munthu woipa,+ koma iye osasiya zoipa zakezo ndi njira zake zoipa, munthuyo adzafa chifukwa cha zoipa zake.+ Koma iweyo udzakhala utapulumutsa moyo wako.+
19 Koma iweyo ukachenjeza munthu woipa,+ koma iye osasiya zoipa zakezo ndi njira zake zoipa, munthuyo adzafa chifukwa cha zoipa zake.+ Koma iweyo udzakhala utapulumutsa moyo wako.+