Yoswa 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kefara-amoni, Ofini, ndi Geba.+ Mizinda 12 ndi midzi yake. Yoswa 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto,