Salimo 121:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Amene akuyang’anira Isiraeli,+Sangawodzere kapena kugona.+ Salimo 135:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Makutu ali nawo koma satha kumva.+Komanso m’mphuno mwawo mulibe mpweya.+ Yesaya 40:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi iwe sukudziwa kapena kodi sunamve?+ Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, ndiye Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angadziwe zimene iyeyo amazimvetsa.+
28 Kodi iwe sukudziwa kapena kodi sunamve?+ Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, ndiye Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angadziwe zimene iyeyo amazimvetsa.+