-
1 Mafumu 18:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Tsopano iwowo apeze ng’ombe zamphongo ziwiri zing’onozing’ono. Asankhepo ng’ombe imodzi n’kuiduladula. Ndiyeno aiike pankhuni koma asayatsepo moto. Ineyo ndikonza ng’ombe inayo n’kuiika pankhuni, koma sindiyatsapo moto.
-