Yona 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova Mulungu anameretsa chomera cha mtundu wa mphonda kuti chiyange pamene Yona anakhala ndi kum’chitira mthunzi. Anachita zimenezi kuti amupulumutse ku masautso ake.+ Yona anasangalala kwambiri chifukwa cha chomeracho.
6 Ndiyeno Yehova Mulungu anameretsa chomera cha mtundu wa mphonda kuti chiyange pamene Yona anakhala ndi kum’chitira mthunzi. Anachita zimenezi kuti amupulumutse ku masautso ake.+ Yona anasangalala kwambiri chifukwa cha chomeracho.