1 Mafumu 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kuti akamuuze kuti: “Milungu yanga indilange+ mowirikiza,+ ngati pofika nthawi ino mawa sindidzachititsa moyo wako kukhala ngati moyo wa aliyense wa aneneriwo.” Yeremiya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi ndingakukhululukire bwanji zinthu zimenezi? Ana ako aamuna andisiya ndipo amalumbira+ pa zinthu zina osati Mulungu.+ Ndinali kuwapatsa zofuna zawo+ koma anapitiriza kuchita chigololo+ ndipo anali kupita kunyumba ya hule m’magulumagulu.
2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kuti akamuuze kuti: “Milungu yanga indilange+ mowirikiza,+ ngati pofika nthawi ino mawa sindidzachititsa moyo wako kukhala ngati moyo wa aliyense wa aneneriwo.”
7 Kodi ndingakukhululukire bwanji zinthu zimenezi? Ana ako aamuna andisiya ndipo amalumbira+ pa zinthu zina osati Mulungu.+ Ndinali kuwapatsa zofuna zawo+ koma anapitiriza kuchita chigololo+ ndipo anali kupita kunyumba ya hule m’magulumagulu.