Deuteronomo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Pakuti dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu, si lofanana ndi dziko la Iguputo limene munatulukamo. Kumeneko munali kufesa mbewu zanu ndi kuzithirira ndi mapazi* anu, ngati kuti mukuthirira dimba la ndiwo zamasamba.
10 “Pakuti dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu, si lofanana ndi dziko la Iguputo limene munatulukamo. Kumeneko munali kufesa mbewu zanu ndi kuzithirira ndi mapazi* anu, ngati kuti mukuthirira dimba la ndiwo zamasamba.