Deuteronomo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Usagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wako mosasamala,+ pakuti Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake mosasamala osam’langa.+ 2 Mbiri 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno mfumuyo inamuuza kuti: “Kodi ndikulumbiritse kangati+ kuti uzilankhula kwa ine zoona zokhazokha m’dzina la Yehova?”+
11 “‘Usagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wako mosasamala,+ pakuti Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake mosasamala osam’langa.+
15 Ndiyeno mfumuyo inamuuza kuti: “Kodi ndikulumbiritse kangati+ kuti uzilankhula kwa ine zoona zokhazokha m’dzina la Yehova?”+