Miyambo 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+
21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+