1 Mbiri 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Zera+ anali Zimiri, Etani, Hemani, Kalikoli, ndi Dara.+ Onse pamodzi analipo asanu.