1 Mafumu 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Solomo, m’mwezi wa Zivi,+ anamanga maziko+ a nyumba ya Yehova. 1 Mbiri 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+
37 M’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Solomo, m’mwezi wa Zivi,+ anamanga maziko+ a nyumba ya Yehova.
19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+