Genesis 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chingalawacho uchiike windo.* Windolo likhale la mpata wa mkono umodzi kuchokera kudenga* lake. Khomo la chingalawacho uliike m’mbali mwake.+ Chikhale cha nyumba zosanjikiza zitatu, yapansi, yapakati, ndi yapamwamba.
16 Chingalawacho uchiike windo.* Windolo likhale la mpata wa mkono umodzi kuchokera kudenga* lake. Khomo la chingalawacho uliike m’mbali mwake.+ Chikhale cha nyumba zosanjikiza zitatu, yapansi, yapakati, ndi yapamwamba.