1 Mafumu 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakhomo la chipinda chamkati anaikapo zitseko+ za mtengo wamafuta,+ zipilala za m’mbali, ndi mafelemu. Zimenezi zinali mbali yachisanu.
31 Pakhomo la chipinda chamkati anaikapo zitseko+ za mtengo wamafuta,+ zipilala za m’mbali, ndi mafelemu. Zimenezi zinali mbali yachisanu.