1 Mbiri 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu okhala ku Yebusiwo anayamba kuuza Davide kuti: “Sulowa mumzinda uno.”+ Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni,+ malo okhala mumpanda wolimba kwambiri, umene ndi Mzinda wa Davide.+
5 Anthu okhala ku Yebusiwo anayamba kuuza Davide kuti: “Sulowa mumzinda uno.”+ Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni,+ malo okhala mumpanda wolimba kwambiri, umene ndi Mzinda wa Davide.+