2 Mbiri 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero, Solomo anabwerera ku Yerusalemu kuchokera kumalo okwezeka a ku Gibeoni,+ kuchihema chokumanako,+ ndipo anapitiriza kulamulira Isiraeli.+
13 Zitatero, Solomo anabwerera ku Yerusalemu kuchokera kumalo okwezeka a ku Gibeoni,+ kuchihema chokumanako,+ ndipo anapitiriza kulamulira Isiraeli.+