Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere: 1 Mbiri 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide atamaliza kupereka nsembe yopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano,+ anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova.+ 2 Mbiri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako mfumu inatembenuka n’kuyang’ana anthuwo. Ndiyeno inayamba kudalitsa+ mpingo wonse wa Isiraeli. Pamenepo n’kuti mpingo wonse wa Isiraeli utaimirira.+
2 Davide atamaliza kupereka nsembe yopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano,+ anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova.+
3 Kenako mfumu inatembenuka n’kuyang’ana anthuwo. Ndiyeno inayamba kudalitsa+ mpingo wonse wa Isiraeli. Pamenepo n’kuti mpingo wonse wa Isiraeli utaimirira.+