2 Mbiri 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Solomo anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli.+ Kenako anatambasula manja ake.+
12 Tsopano Solomo anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli.+ Kenako anatambasula manja ake.+