2 Mbiri 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano chikhamu cha anthu chinasonkhana ku Yerusalemu+ kuti achite chikondwerero+ cha mkate wopanda chofufumitsa m’mwezi wachiwiri,+ ndipo unali mpingo waukulu kwambiri. Salimo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+
13 Tsopano chikhamu cha anthu chinasonkhana ku Yerusalemu+ kuti achite chikondwerero+ cha mkate wopanda chofufumitsa m’mwezi wachiwiri,+ ndipo unali mpingo waukulu kwambiri.
9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+