1 Mafumu 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ahisara anali woyang’anira banja lachifumu, ndipo Adoniramu,+ mwana wa Abada, anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+ 1 Mafumu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu amene Mfumu Solomo inawalemba ntchito yokakamiza anachokera ku Isiraeli konse, ndipo anthu olembedwa ntchito yokakamizawo+ anakwana amuna 30,000.
6 Ahisara anali woyang’anira banja lachifumu, ndipo Adoniramu,+ mwana wa Abada, anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+
13 Anthu amene Mfumu Solomo inawalemba ntchito yokakamiza anachokera ku Isiraeli konse, ndipo anthu olembedwa ntchito yokakamizawo+ anakwana amuna 30,000.