2 Mbiri 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mfumu Solomo inapatsa mfumukazi+ ya ku Sheba zofuna zake zonse zimene inapempha. Solomo anapatsa mfumukaziyo zinthu zoposa zimene inabweretsa kwa iye. Pambuyo pake, mfumukaziyo inatembenuka n’kubwerera kudziko lake, pamodzi ndi antchito ake.+
12 Mfumu Solomo inapatsa mfumukazi+ ya ku Sheba zofuna zake zonse zimene inapempha. Solomo anapatsa mfumukaziyo zinthu zoposa zimene inabweretsa kwa iye. Pambuyo pake, mfumukaziyo inatembenuka n’kubwerera kudziko lake, pamodzi ndi antchito ake.+