2 Mbiri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+
16 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+