2 Samueli 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wachinayi anali Adoniya+ wobadwa kwa Hagiti,+ ndipo wachisanu anali Sefatiya+ wobadwa kwa Abitali.